Mateyu 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Pilato anamufunsa kuti: “Kodi sukumva zonse zimene akukunenezazi?”+ Yohane 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”
10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”