Luka 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu anangoima chilili kuonerera zochitikazo.+ Koma olamulira anali kumunyogodola kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, m’lekeni adzipulumutse yekha,+ ngati iyeyu alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+
35 Anthu anangoima chilili kuonerera zochitikazo.+ Koma olamulira anali kumunyogodola kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, m’lekeni adzipulumutse yekha,+ ngati iyeyu alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+