-
Yohane 20:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma Mariya anatsala atangoima panja pafupi ndi manda achikumbutsowo akulira. Akulira choncho, anawerama kuti aone m’manda achikumbutsowo.
-