Luka 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi simunawerenge kuti analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kutenga mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu+ n’kudya, ndipo ina anapatsa amuna amene anali naye limodzi? Malamulo salola aliyense kudya mkate umenewu koma ansembe okha.”+
4 Kodi simunawerenge kuti analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kutenga mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu+ n’kudya, ndipo ina anapatsa amuna amene anali naye limodzi? Malamulo salola aliyense kudya mkate umenewu koma ansembe okha.”+