Salimo 51:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti zolakwa zanga ndikuzidziwa bwino,+Ndipo tchimo langa lili pamaso panga nthawi zonse.+