1 Akorinto 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+ 1 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma monga makanda obadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasukuluka+ umene uli m’mawu a Mulungu, kuti mwa kumwa mkakawo, mukule ndi kukhala oyenera chipulumutso,+
20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+
2 Koma monga makanda obadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasukuluka+ umene uli m’mawu a Mulungu, kuti mwa kumwa mkakawo, mukule ndi kukhala oyenera chipulumutso,+