Mateyu 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndi kunena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Mukapanda kutembenuka n’kukhala ngati ana aang’ono,+ simudzalowa mu ufumu wakumwamba.+ Maliko 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndithu ndikukuuzani, Aliyense wosalandira ufumu wa Mulungu ngati mwana wamng’ono sadzalowa n’komwe mu ufumuwo.”+
3 ndi kunena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Mukapanda kutembenuka n’kukhala ngati ana aang’ono,+ simudzalowa mu ufumu wakumwamba.+
15 Ndithu ndikukuuzani, Aliyense wosalandira ufumu wa Mulungu ngati mwana wamng’ono sadzalowa n’komwe mu ufumuwo.”+