-
Mateyu 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mnyamatayo anayankha Yesu kuti: “Ndakhala ndikutsatira zonsezi, n’chiyaninso chimene ndikupereweza?”
-
-
Maliko 10:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pamenepo munthuyo anayankha kuti: “Mphunzitsi, zonsezi ndakhala ndikuzitsatira kuyambira ndili wamng’ono.”
-