Luka 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndipo mwanayo anali kukulirakulira ndi kukhala wamphamvu.+ Nzeru zake zinali kuchuluka ndipo Mulungu anapitiriza kukondwera naye.+
40 Ndipo mwanayo anali kukulirakulira ndi kukhala wamphamvu.+ Nzeru zake zinali kuchuluka ndipo Mulungu anapitiriza kukondwera naye.+