Mateyu 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kuyambira pamenepo, Yesu Khristu anayamba kuuza ophunzira ake kuti n’koyenera kuti iye apite ku Yerusalemu. Kumeneko akazunzidwa kwambiri ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno akaphedwa, koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.+ Maliko 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano anapitiriza ulendo wawo wopita ku Yerusalemu. Yesu anali patsogolo pawo, ndipo iwo anadabwa kwambiri. Anthu amene anali kum’tsatirawo anayamba kuchita mantha. Pamenepanso anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuyamba kuwauza zinthu izi zimene zinali pafupi kum’chitikira:+
21 Kuyambira pamenepo, Yesu Khristu anayamba kuuza ophunzira ake kuti n’koyenera kuti iye apite ku Yerusalemu. Kumeneko akazunzidwa kwambiri ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno akaphedwa, koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.+
32 Tsopano anapitiriza ulendo wawo wopita ku Yerusalemu. Yesu anali patsogolo pawo, ndipo iwo anadabwa kwambiri. Anthu amene anali kum’tsatirawo anayamba kuchita mantha. Pamenepanso anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuyamba kuwauza zinthu izi zimene zinali pafupi kum’chitikira:+