Danieli 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Pamalo pake padzauka wina+ amene adzachititsa wokhometsa msonkho*+ kuyendayenda mu ufumu waulemererowo, ndipo m’masiku ochepa adzathyoka, koma osati ndi dzanja la munthu kapena pa nkhondo.
20 “Pamalo pake padzauka wina+ amene adzachititsa wokhometsa msonkho*+ kuyendayenda mu ufumu waulemererowo, ndipo m’masiku ochepa adzathyoka, koma osati ndi dzanja la munthu kapena pa nkhondo.