Maliko 10:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Choncho, Yesu anaima ndi kunena kuti: “Muitaneni.” Iwo anaitana wakhunguyo, ndi kumuuza kuti: “Limba mtima, nyamuka, akukuitana.”+
49 Choncho, Yesu anaima ndi kunena kuti: “Muitaneni.” Iwo anaitana wakhunguyo, ndi kumuuza kuti: “Limba mtima, nyamuka, akukuitana.”+