Maliko 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ena mwa anthu amene anali ataimirira chapomwepo anayamba kuwafunsa kuti: “Cholinga chanu n’chiyani pomasula buluyu?”+
5 Koma ena mwa anthu amene anali ataimirira chapomwepo anayamba kuwafunsa kuti: “Cholinga chanu n’chiyani pomasula buluyu?”+