Luka 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anamutumiza kwa namwali amene mwamuna wina wotchedwa Yosefe, wa m’nyumba ya Davide, anamulonjeza kuti adzamukwatira. Namwali+ ameneyu dzina lake anali Mariya.+
27 Anamutumiza kwa namwali amene mwamuna wina wotchedwa Yosefe, wa m’nyumba ya Davide, anamulonjeza kuti adzamukwatira. Namwali+ ameneyu dzina lake anali Mariya.+