Maliko 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anayamba kum’funsa kuti: “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Machitidwe 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anaimika atumwiwo pakati pawo n’kuyamba kuwafunsa kuti: “Kodi mwachita zimenezi ndi ulamuliro uti kapena m’dzina la ndani?”+ Machitidwe 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma amene anali kuzunza mnzakeyo anamukankha ndi kunena kuti, ‘Iweyo anakuika ndani kuti ukhale wolamulira ndi woweruza wathu?+
28 Iwo anayamba kum’funsa kuti: “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+
7 Ndiyeno anaimika atumwiwo pakati pawo n’kuyamba kuwafunsa kuti: “Kodi mwachita zimenezi ndi ulamuliro uti kapena m’dzina la ndani?”+
27 Koma amene anali kuzunza mnzakeyo anamukankha ndi kunena kuti, ‘Iweyo anakuika ndani kuti ukhale wolamulira ndi woweruza wathu?+