Maliko 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo m’nyumba imene akalowe, mukauze mwininyumbayo kuti, ‘Mphunzitsi akufunsa kuti: “Chipinda cha alendo chili kuti, mmene ine ndidyeremo pasika+ pamodzi ndi ophunzira anga?”’+
14 ndipo m’nyumba imene akalowe, mukauze mwininyumbayo kuti, ‘Mphunzitsi akufunsa kuti: “Chipinda cha alendo chili kuti, mmene ine ndidyeremo pasika+ pamodzi ndi ophunzira anga?”’+