Mateyu 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamene anali kudya, iye anati: “Ndithu ndikukuuzani, Mmodzi wa inu andipereka.”+ Yohane 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atanena zimenezi, Yesu anasautsika mu mzimu, ndipo anachitira umboni kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mmodzi wa inu andipereka.”+
21 Atanena zimenezi, Yesu anasautsika mu mzimu, ndipo anachitira umboni kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mmodzi wa inu andipereka.”+