Maliko 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwo anangokhala chete, pakuti m’njira anali kukangana za amene ali wamkulu pakati pawo.+ Luka 9:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako iwo anayamba kukhala ndi maganizo ofuna kudziwa amene ali wamkulu koposa pakati pawo.+