Yohane 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Moyo wanga ukusautsika tsopano,+ ndinene chiyani kodi? Atate ndipulumutseni ku nthawi yosautsayi.+ Komabe nthawi imeneyi iyenera kundifikira pakuti ndiye chifukwa chake ndinabwera. Aheberi 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+
27 Moyo wanga ukusautsika tsopano,+ ndinene chiyani kodi? Atate ndipulumutseni ku nthawi yosautsayi.+ Komabe nthawi imeneyi iyenera kundifikira pakuti ndiye chifukwa chake ndinabwera.
7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+