-
Luka 22:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Pamenepo anawauza kuti: “Koma tsopano amene ali ndi chikwama cha ndalama achitenge, chimodzimodzinso thumba la chakudya. Ndipo amene alibe lupanga agulitse malaya ake akunja n’kugula lupanga.
-