Yohane 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?”
11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?”