Yohane 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akapolo ndi alonda anali ataima chapomwepo, pakuti anali atakoleza moto wamakala,+ chifukwa kunali kuzizira ndipo anali kuwotha motowo. Nayenso Petulo anaimirira pamodzi ndi iwo n’kumawotha nawo.
18 Akapolo ndi alonda anali ataima chapomwepo, pakuti anali atakoleza moto wamakala,+ chifukwa kunali kuzizira ndipo anali kuwotha motowo. Nayenso Petulo anaimirira pamodzi ndi iwo n’kumawotha nawo.