Mateyu 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+ Maliko 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwamsanga m’bandakucha, ansembe aakulu, akulu ndi alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi ndi kugwirizana chimodzi.+ Kenako anamanga Yesu ndi kukam’pereka kwa Pilato.+
27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+
15 Mwamsanga m’bandakucha, ansembe aakulu, akulu ndi alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi ndi kugwirizana chimodzi.+ Kenako anamanga Yesu ndi kukam’pereka kwa Pilato.+