Salimo 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikuikiza mzimu* wanga m’manja mwanu.+Mwandiwombola,+ inu Yehova, Mulungu wachoonadi.+ Machitidwe 7:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+
59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+