Mateyu 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kunafika mayi wina ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala muli mafuta onunkhira okwera mtengo.+ Mayiyo atayandikira Yesu, anayamba kumuthira mafutawo m’mutu pamene iye anali kudya patebulo.
7 kunafika mayi wina ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala muli mafuta onunkhira okwera mtengo.+ Mayiyo atayandikira Yesu, anayamba kumuthira mafutawo m’mutu pamene iye anali kudya patebulo.