Yohane 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho pamene anauka kwa akufa, ophunzira ake anakumbukira+ kuti anali kunena zimenezi, ndipo anakhulupirira Malemba ndi mawu amene Yesu ananena.
22 Choncho pamene anauka kwa akufa, ophunzira ake anakumbukira+ kuti anali kunena zimenezi, ndipo anakhulupirira Malemba ndi mawu amene Yesu ananena.