Mateyu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+ Luka 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’mwezi wake wa 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa Galileya, wotchedwa Nazareti.
23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+
26 M’mwezi wake wa 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa Galileya, wotchedwa Nazareti.