Mateyu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene Yohane anaona Afarisi ndi Asaduki+ ambiri akubwera ku ubatizowo, anawauza kuti: “Ana a njoka inu,+ ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+ Mateyu 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Njoka inu, ana a mphiri,+ mudzathawa bwanji chiweruzo cha Gehena?+
7 Pamene Yohane anaona Afarisi ndi Asaduki+ ambiri akubwera ku ubatizowo, anawauza kuti: “Ana a njoka inu,+ ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+