Machitidwe 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano iwo atamva mawu amenewa, anavutika kwambiri mumtima,+ ndipo anafunsa Petulo ndi atumwi enawo kuti: “Amuna inu, abale athu, tichite chiyani pamenepa?”+ Machitidwe 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anawatulutsa kunja n’kunena kuti: “Mabwana inu, ndichite chiyani+ kuti ndipulumuke?”
37 Tsopano iwo atamva mawu amenewa, anavutika kwambiri mumtima,+ ndipo anafunsa Petulo ndi atumwi enawo kuti: “Amuna inu, abale athu, tichite chiyani pamenepa?”+