Yohane 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho anamufunsa kuti: “Ngati iweyo sindiwe Khristu, kapena Eliya, kapenanso Mneneri, nanga n’chifukwa chiyani umabatiza anthu?”+
25 Choncho anamufunsa kuti: “Ngati iweyo sindiwe Khristu, kapena Eliya, kapenanso Mneneri, nanga n’chifukwa chiyani umabatiza anthu?”+