Genesis 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60. 1 Mbiri 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Awa ndiwo anali ana a Isiraeli:+ Rubeni,+ Simiyoni,+ Levi,+ Yuda,+ Isakara,+ Zebuloni,+
26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.