Deuteronomo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Musamuyese, Yehova Mulungu wanu,+ mmene munamuyesera pa Masa.*+ 1 Akorinto 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kapena tisamuyese Yehova,+ mmene ena mwa iwo anamuyesera,+ n’kuwonongeka polumidwa ndi njoka.+