Luka 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndithudi ndikukuuzani, Mwa onse obadwa mwa akazi, palibe wamkulu+ woposa Yohane. Koma munthu amene ali wocheperapo mu ufumu wa Mulungu ndiye wamkulu kuposa iyeyu.”+
28 Ndithudi ndikukuuzani, Mwa onse obadwa mwa akazi, palibe wamkulu+ woposa Yohane. Koma munthu amene ali wocheperapo mu ufumu wa Mulungu ndiye wamkulu kuposa iyeyu.”+