Mateyu 21:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Alimiwo ataona mwanayo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe ndi kutenga cholowa chakecho!’+
38 Alimiwo ataona mwanayo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe ndi kutenga cholowa chakecho!’+