Yakobo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho?+ Ukuchita bwino. Koma ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+
19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho?+ Ukuchita bwino. Koma ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+