Deuteronomo 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ukalowa m’munda wa tirigu wa mnzako, uzipulula ndi dzanja lako tirigu yekhayo amene wacha, koma usamwete tirigu wa mnzako ndi chikwakwa.+
25 “Ukalowa m’munda wa tirigu wa mnzako, uzipulula ndi dzanja lako tirigu yekhayo amene wacha, koma usamwete tirigu wa mnzako ndi chikwakwa.+