Luka 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kanthawi kena atalowa m’nyumba ya mmodzi wa akuluakulu a Afarisi pa sabata kukadya chakudya,+ Afarisiwo anali kumuyang’anitsitsa.+
14 Kanthawi kena atalowa m’nyumba ya mmodzi wa akuluakulu a Afarisi pa sabata kukadya chakudya,+ Afarisiwo anali kumuyang’anitsitsa.+