Luka 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’mwezi wake wa 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa Galileya, wotchedwa Nazareti.
26 M’mwezi wake wa 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa Galileya, wotchedwa Nazareti.