Mateyu 5:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pakuti mukamakonda anthu okhawo amene amakukondani, kodi mudzalandira mphoto yotani?+ Kodi okhometsa msonkho sachitanso zimenezo? 1 Timoteyo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira,+ makamaka a m’banja lake,+ wakana+ chikhulupiriro+ ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.
46 Pakuti mukamakonda anthu okhawo amene amakukondani, kodi mudzalandira mphoto yotani?+ Kodi okhometsa msonkho sachitanso zimenezo?
8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira,+ makamaka a m’banja lake,+ wakana+ chikhulupiriro+ ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.