Mateyu 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Wophunzira saposa mphunzitsi wake, ndipo kapolo saposa mbuye wake.+ Yohane 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndithudi ndikukuuzani, Kapolo saposa mbuye wake, ndiponso wotumidwa saposa amene wamutuma.+ Yohane 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbukirani mawu amene ndinakuuzani aja, kapolo sali wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso anu.
20 Kumbukirani mawu amene ndinakuuzani aja, kapolo sali wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso anu.