-
Luka 1:65Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
65 Pamenepo onse okhala moyandikana nawo anagwidwa mantha. Ndipo nkhani imeneyi inali m’kamwam’kamwa m’madera onse a kumapiri a Yudeya.
-