Mateyu 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma pamene Yohane anali m’ndende, anamva+ zimene Khristu anali kuchita, ndipo anatuma ophunzira ake Yohane 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo anafika kwa Yohane ndi kumuuza kuti: “Rabi, munthu amene munali naye kutsidya kwa Yorodano uja, amene munali kumuchitira umboni uja,+ iyenso akubatiza ndipo anthu onse akupita kwa iye.”+
2 Koma pamene Yohane anali m’ndende, anamva+ zimene Khristu anali kuchita, ndipo anatuma ophunzira ake
26 Pamenepo anafika kwa Yohane ndi kumuuza kuti: “Rabi, munthu amene munali naye kutsidya kwa Yorodano uja, amene munali kumuchitira umboni uja,+ iyenso akubatiza ndipo anthu onse akupita kwa iye.”+