Mateyu 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anali kuwabatiza mumtsinje wa Yorodano,+ ndipo anthuwo anali kuulula machimo awo poyera. Luka 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Okhometsa msonkho nawonso anabwera kudzabatizidwa, ndipo anali kumufunsa kuti: “Mphunzitsi, tichite chiyani?”+
12 Okhometsa msonkho nawonso anabwera kudzabatizidwa, ndipo anali kumufunsa kuti: “Mphunzitsi, tichite chiyani?”+