Mateyu 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amene ali ndi makutu amve.+ Mateyu 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene ali ndi makutu amve.”+ Maliko 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anawonjezera mawu akuti: “Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+