Mateyu 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ophunzira ake anabwera ndi kum’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukulankhula nawo mwa mafanizo?”+ Maliko 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano pamene anakhala payekha, ena amene anali naye chapafupi limodzi ndi atumwi 12 aja, anayamba kum’funsa za mafanizo aja.+
10 Tsopano ophunzira ake anabwera ndi kum’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukulankhula nawo mwa mafanizo?”+
10 Tsopano pamene anakhala payekha, ena amene anali naye chapafupi limodzi ndi atumwi 12 aja, anayamba kum’funsa za mafanizo aja.+