Mateyu 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atafika kutsidya linalo, m’dera la Agadara,+ anakumana ndi amuna awiri ogwidwa ndi ziwanda+ akuchokera m’manda achikumbutso. Amunawa anali ochititsa mantha nthawi zonse moti panalibe aliyense woyesa dala kudutsa msewu umenewo. Maliko 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anafika kutsidya lina la nyanja, m’dera la Agerasa.+
28 Atafika kutsidya linalo, m’dera la Agadara,+ anakumana ndi amuna awiri ogwidwa ndi ziwanda+ akuchokera m’manda achikumbutso. Amunawa anali ochititsa mantha nthawi zonse moti panalibe aliyense woyesa dala kudutsa msewu umenewo.