Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 15:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “‘Mkazi akakha magazi kwa masiku ambiri+ pamene si nthawi yake yokhala wodetsedwa chifukwa cha kusamba,+ kapena akapitiriza kukha magazi nthawi yake yokhala wodetsedwa chifukwa cha kusamba kwake itatha, masiku onse pamene iye akukha magaziwo azikhala ngati mmene amakhalira pa nthawi yake yokhala wodetsedwa chifukwa cha kusamba. Iye ndi wodetsedwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena