Mateyu 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?”+ Maliko 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno anafunsa ophunzirawo kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Poyankha, Petulo ananena kuti: “Ndinu Khristu.”+
29 Ndiyeno anafunsa ophunzirawo kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Poyankha, Petulo ananena kuti: “Ndinu Khristu.”+