Maliko 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Aliyense wolandira mmodzi wa ana aang’ono oterewa m’dzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine, salandira ine ndekha, koma amalandiranso iye amene anandituma.”+ Yohane 12:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma Yesu anafuula kuti: “Wokhulupirira ine sakhulupirira ine ndekha, komanso amakhulupirira iye amene anandituma ine.+
37 “Aliyense wolandira mmodzi wa ana aang’ono oterewa m’dzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine, salandira ine ndekha, koma amalandiranso iye amene anandituma.”+
44 Koma Yesu anafuula kuti: “Wokhulupirira ine sakhulupirira ine ndekha, komanso amakhulupirira iye amene anandituma ine.+