Luka 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma panafika Msamariya+ wina amene anali kudutsanso msewu umenewo. Ndipo atamuona, anagwidwa chifundo. Luka 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atafika anagwada pamaso pa Yesu n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo anamuthokoza. Munthu ameneyu anali Msamariya.+
33 Koma panafika Msamariya+ wina amene anali kudutsanso msewu umenewo. Ndipo atamuona, anagwidwa chifundo.
16 Atafika anagwada pamaso pa Yesu n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo anamuthokoza. Munthu ameneyu anali Msamariya.+